Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zinthu zina zimene mungachite kuti muthetse vuto loseweretsa maliseche, onani nkhani yakuti, “Zimene Achinyamata Amadzifunsa . . . Kodi Ndingathetse Bwanji Chizolowezi Chimenechi?” mu Galamukani! ya November 2006, ndiponso buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Loyamba, patsamba 178 mpaka 182.