Mawu a M'munsi
a Nthawi zinanso Mkhristu angapalamule mlandu waukulu kwa Mkhristu mnzake monga kugwirira, kumenya munthu, kupha, kapena kuba zinthu zochuluka. Zimenezi zikachitika, sikulakwa kuti Mkhristu akanene kupolisi, ngakhale kuti kuchita zimenezi kungachititse kuti wolakwayo aimbidwe mlandu kukhoti.