Mawu a M'munsi
a Ngati mukuzunzidwa ndi bambo kapena mayi amene amaledzera, mungachite bwino kuuza munthu wina wachikulire amene mumam’khulupirira kwambiri kuti akuthandizeni. Ngati ndinu wa Mboni za Yehova, mungauze mkulu mumpingo kapena Mkhristu wina wachikulire.