Mawu a M'munsi
c Ngati mumachita manyazi kulankhula ndi anthu akuluakulu maso ndi maso, mungathe kungowalembera kalata kapena kuwaimbira foni. Nthawi zambiri kuuza ena mmene mukumvera ndi njira yabwino yokuthandizani kuti musamangokhalira kukhumudwa.