Mawu a M'munsi
a Ameneyu si mtumwi Filipo ayi. Koma ndi yemwe, mogwirizana ndi Mutu 5 wa buku lino, anatchulidwa kuti anali m’gulu la ‘amuna 7 a mbiri yabwino,’ amene anapatsidwa udindo woyang’anira ntchito yogawa chakudya tsiku ndi tsiku kwa akazi amasiye olankhula Chigiriki komanso olankhula Chiheberi ku Yerusalemu.—Mac. 6:1-6.