Mawu a M'munsi
e Pochita kafukufukuyu, anapeza kuti zinthu zikasinthidwa zinali zosatheka kuti zinthuzo zizisinthabe. Pa zomera 100 zimene ankazisintha, chimodzi chokha n’chimene chinkasankhidwa kuti ayese kuchisinthanso. Pa zomwe zinasankhidwazo, anapezanso kuti chimodzi pa 100, n’chimene chikanatha kuyenda malonda. Koma sanakwanitse kupanga ngakhale mtundu umodzi watsopano wa zomera. Atayesa kuchita zimenezi ndi nyama, zotsatira zake zinali zoipa kwambiri kuyerekezera ndi zimene anapeza posintha zomera, moti anangosiya kuchita kafukufuku wa zinyamazo.