Mawu a M'munsi
f Ngakhale zinthu zakufa zochepa zimene asayansi amagwiritsa ntchito kuti apereke umboni wakuti zamoyo zinasintha kuchokera ku zinthu zina ndi zokayikitsa. Onani tsamba 22 mpaka 29 la kabuku kakuti Mmene Moyo Unayambira—Mafunso 5 Ofunika Kwambiri kolembedwa ndi Mboni za Yehova.