Mawu a M'munsi
a Pofotokoza zimene zinachitika pa “tsiku” loyamba, anagwiritsa ntchito mawu achiheberi akuti ‘ohr amene amanena za kuwala basi. Koma pofotokoza za “tsiku” la 4, anagwiritsa ntchito mawu oti ma·’ohrʹ omwe amatanthauza kumene kuwalako kumachokera.