Mawu a M'munsi
b Mapulotini ena amene maselo amapanga amakhala maenzayimu. Enzayimu iliyonse imapindidwa munjira yapadera kuti izifulumizitsa zinthu zosiyanasiyana zimene zimachitika muselo. Maenzayimu ambirimbiri amagwira ntchito limodzi pothandiza kuti ntchito za muselo ziziyenda bwino.