Mawu a M'munsi c Maselo ena m’thupi la munthu amapangidwa ndi mamolekyu a pulotini pafupifupi 10 biliyoni11 ndipo amakhala amitundu yosiyanasiyana yokwana masauzande ambiri.12