Mawu a M'munsi
a Chifukwa chakuti ndife ochimwa aliyense amalakwitsa zinthu. (Aroma 3:23) Choncho, mnzanu akachita zinthu zokukhumudwitsani n’kupepesa kuchokera pansi pamtima, muzikumbukira mfundo yakuti: “Chikondi chimakwirira machimo ochuluka.”—1 Petulo 4:8.