Mawu a M'munsi
a N’zoona kuti anthu ambiri amadwala matenda osiyanasiyana komanso ena ndi olumala ndipo palibe chimene angachite kuti athetse vuto lawolo. Mutu uno wakonzedwa n’cholinga chothandiza anthu oterewa kuti akhale ndi thanzi labwinoko malinga ndi zimene angathe.