Mawu a M'munsi a Achinyamata ena akavutika maganizo kwa nthawi yaitali amafuna kungodzipha. Ngati munakhalapo ndi maganizo amenewa, fotokozerani munthu wina wamkulu amene mumam’khulupirira.—Kuti mudziwe zambiri, onani Mutu 14.