Mawu a M'munsi a “Mkazi wabwino” wotchulidwa pa Miyambo 31:10-28 amaoneka kuti anali ndi maudindo angapo akuluakulu okhudza za ndalama. Onani vesi 13, 14, 16, 18 ndi 24.