Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, “Ndiziyesetsa kupewa kugonana ndi munthu mpaka ndidzalowe m’banja ndipo ndikukhulupirira kuti kuchita zimenezi ndi nzeru chifukwa . . .” Onetsetsani kuti mwalemba zimene inuyo mwasankha kuchita osati kungotengera wina.