Mawu a M'munsi
a Samueli anapha Agagi. Mfumu imeneyi ngakhalenso anthu a m’banja lake sankafunika kuchitiridwa chifundo. Ziyenera kuti patapita zaka zambiri, mbadwa za Agagi zinaphatikizapo “Hamani Mwagagi” yemwe ankafuna kupha atumiki onse a Mulungu.—Esitere 8:3; onani Mutu 15 ndi 16 m’buku lino.