Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

c N’zochititsa chidwi kuti Eliya anawauza kuti: “Musayatse moto” pa nsembeyo. Akatswiri ena a Baibulo amati opembedza mafano amenewa nthawi zina ankagwiritsa ntchito maguwa ansembe amene ankakhala ndi bowo kunsi kumene ankabisako moto. Iwo ankachita zimenezi n’cholinga choti anthu aziona ngati milungu yawo ndi imene yayatsa motowo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena