Mawu a M'munsi a Umboni woti anthuwa anali osachedwa kusintha maganizo umaoneka tikayerekezera zimene iwo ananena pa nthawiyi ndi zimene ananena dzulo lake, pamene ananena mosangalala kuti Yesu ndi mneneri wa Mulungu.—Yoh. 6:14.