Mawu a M'munsi
b Kuchokera kugombe la nyanja ya Galileya, gululi linayenda ulendo wa makilomita pafupifupi 45. Iwo anachoka kugombe lotsika kwambiri ndipo anadutsa m’dera lokongola kukafika kumalo okwera kwambiri.