Mawu a M'munsi
a Dzina la Mulungu likuchokera ku mawu achiheberi amene amatanthauza “kukhala.” Dzina lakuti Yehova limasonyeza kuti iye amachititsa kuti malonjezo ake akwaniritsidwe. Onani bokosi lakuti, “Tanthauzo la Dzina la Mulungu,” patsamba 43.