Mawu a M'munsi
b Ngakhale kuti masiku ano nthawi imeneyi ingaoneke ngati yaitali kwambiri, tiyenera kukumbukira kuti anthu akale ankakhala ndi moyo wautali moti panali mibadwo 4 yokha kuchokera pa Adamu kufika pa Abulahamu. Pamene Lameki, bambo ake a Nowa amabadwa n’kuti Adamu adakali ndi moyo. Pamene Semu, mwana wa Nowa amabadwa, n’kuti Lameki adakali ndi moyo. Pamene Abulahamu amabadwa n’kuti Semu adakali ndi moyo.—Gen. 5:5, 31; 9:29; 11:10, 11; 25:7.