Mawu a M'munsi
b Mabuku ena amene athandiza atumiki a Mulungu pophunzitsa anthu ena choonadi cha m’Baibulo ndi Zeze wa Mulungu (linafalitsidwa mu 1921), “Mulungu Akhale Woona” (linafalitsidwa mu 1946), Mungathe Kukhala ndi Moyo Kosatha m’Paradaiso pa Dziko Lapansi (linafalitsidwa mu 1982) ndi lakuti Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha (linafalitsidwa mu 1995).