Mawu a M'munsi c Nkhani imeneyi inanena kuti sizomveka kuti Yesu anabadwa nyengo ya dzinja chifukwa “sizikugwirizana ndi zimene Baibulo limanena kuti pa nthawi imene Yesu amabadwa n’kuti abusa akugonera kubusa ndi nkhosa zawo.”—Luka 2:8.