Mawu a M'munsi
d M’kalata imene M’bale Frederick W. Franz analemba pa November 14, 1927, anati: “Chaka chino sitikhala ndi Khirisimasi. Banja la Beteli lagwirizana kuti tisadzapangenso mwambo wa Khirisimasi mpaka kalekale.” Patangopita miyezi yochepa, pa February 6, 1928, M’bale Franz analembanso kuti: “Ambuye akutiyeretsa pang’onopang’ono kuti tisakhalenso ndi zinthu zochokera ku Babulo yemwe akutsogoleredwa ndi Mdyerekezi.”