Mawu a M'munsi
b Lonjezoli linkaletsa mwamuna ndi mkazi kukhala awiriwiri m’chipinda pokhapokha chitseko chikhale chotsekula kwambiri kapena ngati anthuwo ndi banja kapenanso ndi apachibale chapafupi. Kwa zaka zingapo, anthu a pa Beteli ankaloweza lonjezo limeneli n’kumalinena tsiku lililonse pa kulambira kwa m’mawa.