Mawu a M'munsi
c Katswiri wina wolemba mabuku ananena kuti mawu achigiriki amene anawamasulira kuti “watsimikizira” amatanthauza kuti munthuyo amayamba waganiza kaye. Iye ananenanso kuti: “Ngakhale kuti munthu amasangalalabe ngakhale atapereka osakonzekera, ayenera kuganizira kaye komanso kutsatira dongosolo lake.”—1 Akor. 16:2.