Mawu a M'munsi
a N’zomveka kunena kuti kuwonongedwa kwa “Babulo Wamkulu” kwenikweni kukutanthauza kuwonongedwa kwa mabungwe a chipembedzo, osati kuphedwa kwa anthu onse omwe ali m’chipembedzo chonyenga. Choncho, anthu ambiri amene poyamba anali m’Babulo Wamkulu adzapulumuka kuwonongedwa kumeneku ndipo n’kutheka kuti adzayamba kulankhula zosonyeza kuti asiya zachipembedzo ngati mmene lemba la Zekariya 13:4-6 limafotokozera.