Mawu a M'munsi
a Zimenezi sizikutanthauza kuti anthu amene amafuna kuti musiye kuphunzira Baibulo ndiye kuti akulamuliridwa ndi Satana. Komano Satana ndi “mulungu wa nthawi ino” ndipo “dziko lonse lili m’manja mwa woipayo.” Choncho n’zosadabwitsa kuona anthu ena akuyesetsa kutilepheretsa kutumikira Yehova.—2 Akorinto 4:4; 1 Yohane 5:19.