b Mwachitsanzo, Paulo anafotokoza kwambiri zokhudza mkulu wa ansembe komanso zimene ankachita pa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo. (Aheb. 2:17; 3:1; 4:14-16; 5:1-10; 7:1-17, 26-28; 8:1-6; 9:6-28) Koma masomphenya a Ezekieli sakutchula za mkulu wa ansembe kapena Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo.