Mawu a M'munsi
a Madokotala ambiri amati zidakwa ndi zimene zimavutika kwambiri kudziletsa kuti zisamwe mowa wambiri. Choncho amati njira yabwino kwa anthu oterewa ndi kusiyiratu kumwa mowa.