Mawu a M'munsi
a Kaamba ka chidziŵitso chowonjezereka pa Opus Dei ndi kudziloŵetsamo kwa tchalitchi m’ndale zadziko, onani mabukhu akuti Hot Money and the Politics of Debt, lolembedwa ndi R. T. Naylor, ndi Politics, Power, and the Church, lolembedwa ndi L. Lader.