Mawu a M'munsi
a Akunja akhala akugwiritsira ntchito zofukiza zochokera kumaluŵa kwanthaŵi yaitali m’madzoma awo, koma sikunali kolakwa kuti anthu a Mulungu agwiritsire ntchito zofukiza m’kulambira kowona. (Eksodo 30:1, 7, 8; 37:29; Chivumbulutso 5:8) Onaninso mutu wakuti “Kodi Ndizo Zokometsera Zakulambira Mafano?” mu Galamukani! Yachingelezi ya December 22, 1976.