Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Yesu ndi Yakobo ananena kuti mvula sinagwe m’dzikolo “zaka zitatu ndi miyezi isanu ndi umodzi.” Komabe, Eliya akunenedwa kukhala akuwonekera pamaso pa Ahabu kuti athetse chilalacho ‘m’chaka chachitatu’​—mosakaikira kuyambira kuŵerengera patsiku limene analengeza chilalacho. Chifukwa chake, ayenera kuti anaima pamaso pa Ahabu kwanthaŵi yoyamba pambuyo pa nyengo yaitali yachilala.​—Luka 4:25; Yakobo 5:17; 1 Mafumu 18:1.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena