Mawu a M'munsi a Pamene Luka 3:23 amati: “Yosefe, mwana wa Heli,” mwachiwonekere amatanthauza “mwana” m’lingaliro la kukhala “mpongozi,” popeza kuti Heli anali atate weniweni wa Mariya.—Insight on the Scriptures, Voliyamu 1, tsamba 913-17.