Mawu a M'munsi
a Kwa zaka zambiri akatswiri ena anakaikira kuti Bukhu Lamakedzana la Aleppo linalidi malembo apamanja oikidwa zizindikiro zoƔerengera ndi Ben Asher. Komabe, popeza kuti bukhu lamakedzanalo lakhalapo kuti lifufuzidwe, umboni wakhala ukupezeka wakuti liridi malembo apamanja a Ben Asher otchulidwa ndi Maimonides.