Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

b Aisrayeli anali ozoloŵerana ndi m’chitidwe wakusungunula zitsulo. M’mabwinja mwapezeka ina yamigodi yawo yamkuwa, ndipo mkuwa unasungunulidwa kukonzera milimo ya pakachisi (Yerekezerani ndi 1 Mafumu 7:14-46.) Kukuwonekera kukhala kosatheka kuti mchitidwe wakusungunula zitsulo umenewo ungakhoze kukhala utachitidwa popanda kuchititsa mlingo waung’ono wakuipitsa mu mpangidwe wa utsi, zitoto, ndi nthale, mwinamwake limodzi ndi ziyambukiro zina zosafunika. Komabe, Yehova mwachiwonekere anali wofunitsitsa kulekerera kumlingo waung’ono kuipitsidwa kwa maloŵa akutali okhalidwa mwa patalipatali.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena