Mawu a M'munsi
a Kupenda kosamalitsa kwa mbiriyo kumakana chinenezo chakuti Yefita anapereka nsembe ya munthu ya mwana wake. Onani Insight on the Scriptures, Voliyumu 2, masamba 27-8, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.