Mawu a M'munsi
a Mfundo imeneyi inamveketsedwa bwino pambuyo pake pamene Satana ananena za Yobu mtumiki wa Mulungu kuti: “Khungu kulipa khungu, inde munthu adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wake. Koma tambasulani dzanja lanu, ndi kukhudza fupa lake ndi mnofu wake, ndipo adzakuchitirani mwano pamaso panu.”—Yobu 2:4, 5.