Mawu a M'munsi
b Kuti mupeze zitsanzo za maulosi otero ndi kukwaniritsidwa kwawo, onani mabuku awa Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu?, masamba 117-61; ndi Kukambitsirana za m’Malemba, masamba 54-6, 374-80, 260-8. Onse aŵiri amafalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.