Mawu a M'munsi
b The Catholic Encyclopedia imati: “‘Kuyenera kwaumulungu kwa mafumu’ kumeneku (kosiyana kwambiri ndi chiphunzitso chakuti ulamuliro wonse, kaya wa mfumu kapena lipabuliki, uli wochokera kwa Mulungu), sikunavomerezedwe konse ndi Tchalitchi cha Katolika. Pa Kukonzanso iko kunatenga mtundu wotsutsa kwambiri Chikatolika, mafumu onga Henry VIII, ndi James I, a ku England, akumadzitengera ulamuliro wachikwanekwane wauzimu ndiponso wa boma.”