Mawu a M'munsi
a Umboni wa Baibulo ndiponso wa mbiri umasonya ku kubadwa kwa Yesu Kristu m’chaka cha 2 B.C. Chotero, kaamba ka kulondola, ambiri amasankha kugwiritsira ntchito mawuwo C.E. (Common Era) ndi B.C.E. (Before the Common Era), ndipo umu ndi mmene madeti asonyezedwera m’zofalitsa za Watch Tower Society.