Mawu a M'munsi
a Buku lothirira ndemanga pa Baibulo lakuti Herders Bibelkommentar, ponena za Salmo 103:14, limati: “Adziŵa bwino kuti analenga anthu ndi fumbi la pansi, ndipo adziŵa zofooka ndi mkhalidwe wa kusakhalitsa kwa moyo wawo, kumene kumawatsendereza kwambiri chiyambire pa uchimo woyambirira.”—Kanyenye ngwathu.