Mawu a M'munsi a Kuti mudziŵe Babulo Wamkulu wophiphiritsirayo m’Malemba mwa njira yolondola, onani mitu 33 mpaka 37 ya buku la Revelation—Its Grand Climax At Hand!, lofalitsidwa mu 1988 ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.