Mawu a M'munsi
b Mishnah ndi buku la ndemanga za arabi, lozikidwa pa zimene Ayuda amayesa lamulo lapakamwa. Linalembedwa cha kumapeto kwa zaka za zana lachiŵiri ndi kuchiyambi kwa zaka za zana lachitatu C.E., likumakhala chiyambi cha Talmud. Kuti mupeze chidziŵitso chowonjezera, onani brosha lakuti Will There Ever Be a World Without War? patsamba 10, lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.