Mawu a M'munsi a Kuti mudziŵe zochuluka za ulosi wa Chivumbulutso wonena za Babulo Wamkulu, onani mitu 33 mpaka 37 ya buku lakuti Revelation—Its Grand Climax At Hand!, lofalitsidwa mu 1988 ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.