Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a M’mawu akuti “mbadwo uwu,” mbali yake yotchedwa demonstrative pronoun yakuti houʹtos imafanana ndi mawu akuti “uwu.” Ingatanthauze chinthu chimene chiliko kapena chokhala pamaso pa wolankhulayo. Koma ingakhalenso ndi matanthauzo ena. Exegetical Dictionary of the New Testament (1991) imati: “Liwu lakuti [houʹtos] limasonyeza chinthu chenicheni cha panthaŵiyo. Chotero [aion houʹtos] ndilo ‘dziko limene lilipo tsopano’ . . . ndipo [geneaʹ haute] ndilo ‘mbadwo umene ulipo ndi moyo tsopano’ (chitsanzo, Mat. 12:41f., 45; 24:34).” Dr. George B. Winer akulemba kuti: “Pronauni yakuti [houʹtos] nthaŵi zina imasonyeza nthaŵi yapatali mtsogolo, osati yapafupi, imene, pokhala ndiyo inali nkhani yaikulu, ndiyo inali pafupi kwambiri m’maganizo, ndi imene inali yapanthaŵiyo m’malingaliro a wolemba.”​—A Grammar of the Idiom of the New Testament, 7th edition, 1897.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena