Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, ena angakhale akulimbana ndi chibadwa china choipa chokhomerezeka kwambiri, monga ngati kuchita ukali, kapena kugonjetsa vuto la psotopsoto.—Onani Galamukani! wa July 8, 1988, masamba 11-13; Awake! ya November 8, 1981, masamba 16-20; Mafunso Achichepere Akufunsa—Mayankho Amene Amathandiza, masamba 198-211, zofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.