Mawu a M'munsi
a Lipoti linanena kuti akazi aƔiri ndi ana asanu anapulumuka mwa kubisala. Akaziwo pambuyo pake anasimbira Aroma omwe anawagwirawo zimene zinachitika.