Mawu a M'munsi
b Ndithudi, mofanana ndi mawu ambiri okhala ndi matanthauzo osiyanasiyana, liwu lakuti neʹphesh lilinso ndi matanthauzo ena. Mwachitsanzo, lingatanthauze munthu wamkati, makamaka kunena za mumtima. (1 Samueli 18:1) Lingatanthauzenso moyo umene munthu ali nawo monga sou.—1 Mafumu 17:21-23.