Mawu a M'munsi
b Insight on the Scriptures imati: “Neʹphesh (sou) sikutchulidwa mogwirizana ndi kulengedwa kwa zomera za pa ‘tsiku’ lachitatu la kulenga (Gen. 1:11-13) kapenanso pambuyo pake, popeza zomera zilibe mwazi.”—Lofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.